Isaiah 1:12 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Ndani amakulamulani kuti mubwere nazo zimenezi pamaso panga? Ndani amakuuzani kuti muzipondaponda m'mabwalo a Nyumba yanga?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakudzaonekera inu pamaso pa Ine, ndani wafuna chimenechi m'dzanja lanu, kupondaponda m'mabwalo mwanga?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndani anakulamulirani kuti mubwere nazo pamaso panga? Ndani anakuwuzani kuti muzipondaponda mʼmabwalo a nyumba yanga?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakudzaonekera inu pamaso pa Ine, ndani wafuna cimeneci m'dzanja lanu, kupondaponda m'mabwalo mwanga?