Isaiah 1:22 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iwe Yerusalemu, unali ngati siliva, koma tsopano wasanduka wopandapake. Unali ngati vinyo wabwino, koma tsopano uli ngati vinyo wosakanizika ndi madzi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Siliva wako wasanduka mphala, vinyo wako wasanganizidwa ndi madzi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Siliva wako wasanduka wachabechabe, vinyo wako wabwino wasungunulidwa ndi madzi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Siliva wako wasanduka mphala, vinyo wako wasanganizidwa ndi madzi.