Isaiah 1:25 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndidzatambasula dzanja langa kuti ndilimbane nawe. Ndidzasungunula machimo ako nkuŵachotsa, monga m'mene amachotsera dzimbiri ndi mankhwala.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo ndidzaikanso dzanja langa pa iwe, ndi kukusungunula kukusiyanitsa iwe ndi mphala yako, ndipo ndidzachotsa seta wako wonse:
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndidzatambasula dzanja langa kuti ndilimbane nawe; ndidzasungunula machimo ako nʼkuwachotsa, monga mmene amachotsera dzimbiri ndi mankhwala.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndipo ndidzaikanso dzanja langa pa iwe, ndi kukusungunula kukusiyanitsa iwe ndi mphala yako, ndipo ndidzacotsa seta wako wonse: