Isaiah 1:29 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mudzachita nayo manyazi mitengo ya thundu imene inkakusangalatsani, mudzagwetsa nkhope chifukwa cha minda imene mudaipatula.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa adzakhala ndi manyazi, chifukwa cha mitengo yathundu munaikhumba, ndipo inu mudzagwa nkhope, chifukwa cha minda imene mwaisankha.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Mudzachita nayo manyazi mitengo ya thundu imene inkakusangalatsani; mudzagwetsa nkhope chifukwa cha minda imene munayipatula.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa adzakhala ndi manyazi, cifukwa ca mitengo yathundu munaikhumba, ndipo inu mudzagwa nkhope, cifukwa ca minda imene mwaisankha.