Isaiah 1:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ng'ombe imadziŵa mwini wake, bulu amadziŵa kumene mwini wake amamdyetsera, koma Aisraele sadziŵa, anthu anga samvetsa konse.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ng'ombe idziwa mwini wake, ndi bulu adziwa pomtsekereza: koma Israele sadziwa, anthu anga sazindikira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngʼombe imadziwa mwini wake, bulu amadziwa kumene kuli gome la mbuye wake, koma Israeli sadziwa, anthu anga samvetsa konse.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ng'ombe idziwa mwini wace, ndi buru adziwa pomtsekereza: koma Israyeli sadziwa, anthu anga sazindikira.