Isaiah 1:30 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pakuti mudzafanafana ndi mtengo wa thundu wofota masamba, mudzakhala ngati munda wopanda madzi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa mudzakhala ngati mtengo wathundu, umene tsamba lake linyala, ngatinso munda wopanda madzi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mudzakhala ngati mtengo wa thundu umene masamba ake akufota, mudzakhala ngati munda wopanda madzi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa mudzakhala ngati mtengo wathundu, umene tsamba lace linyala, ngatinso munda wopanda madzi.