Isaiah 10:28 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adani aja akudza afika ku Aiyati. Apyola ku Migironi, aikiza katundu wao ku Mikimasi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Wafika ku Ayati, wapitirira kunka ku Migironi; pa Mikimasi asunga akatundu ake;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Adani alowa mu Ayati apyola ku Migironi; asunga katundu wawo ku Mikimasi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Wafika ku Aiati, wapitirira kunka ku Migroni; pa Mikimasi asunga akatundu ace;