Isaiah 10:29 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adzera pa mpata uja, nagona ku Geba usiku. Anthu a ku Rama akunjenjemera, a ku Gibea, mzinda wa Saulo, athaŵa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
wapita pampata; wagona pa Geba, Rama anthunthumira; Gibea wa Saulo wathawa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Adutsa pa mpata uja, ndipo akuti, “Tikagona ku Geba” Rama akunjenjemera; Gibeya, mzinda wa Saulo ukuthawa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
wapita pampata; wagona pa Geba, Rama anthunthumira; Gibeya wa Sauli wathawa.