Isaiah 10:30 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Lirani mokweza, inu anthu a ku Galimu! Tcherani khutu, inu anthu a ku Laisa! Yankhani, inu a ku Anatoti.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Fuula ndi mau ako iwe mwana wamkazi wa Galimu! Tamva, iwe Laisa! Iwe Anatoti wosauka!
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Lilani mokweza, inu anthu a ku Galimu! Tchera khutu, iwe Laisa! Iwe Anatoti wosauka!
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pfuula ndi mau ako iwe mwana wamkazi wa Galimu! tamva, iwe Laisa! iwe Anatoti wosauka!