Isaiah 10:31 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu a ku Madimena akuthaŵa, a ku Gebimu akubisala.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Madimena ali wothawathawa; okhala m'Gebimu asonkhana kuti athawe.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu a ku Madimena akuthawa; anthu a ku Gebimu bisalani.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Madimena ali wothawathawa; okhala m'Gebimu asonkhanakutiathawe.