Isaiah 10:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta akuti, “Tsoka kwa mfumu ya ku Asiriya, mkwapulo wa ukali wanga, ndodo ya mkwiyo wanga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Iwe Asiriya chibonga cha mkwiyo wanga, ndodo m'dzanja lake muli ukali wanga!
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Tsoka kwa mfumu ya ku Asiriya, chikwapu cha mkwiyo wanga, iye ndiye ndodo ya mkwiyo wanga!
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Iwe Asuri cibonga ca mkwiyo wanga, ndodo m'dzanja lace muli ukali wanga!