Isaiah 10:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma mfumu ya ku Asiriya sikudziŵa zimenezi ndipo mtima wake sukuganiza choncho. Mtima wake uli pa kuwononga ndi kupulula mitundu yochuluka ya anthu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma iye safuna chotero, ndipo mtima wake suganizira chotero, koma mtima wake ulikufuna kusakaza, ndi kuduladula amitundu osawerengeka.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma izi si zimene akufuna kukachita, izi si zimene zili mʼmaganizo mwake; cholinga chake ndi kukawononga, kukapulula mitundu yambiri ya anthu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma iye safuna cotero, ndipo mtima wace suganizira cotero, koma mtima wace ulikufuna kusakaza, ndi kuduladula amitundu osawerengeka.