Isaiah 11:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adzakwezera mitundu ya anthu mbendera, adzasonkhanitsa otayika a ku Israele ndi obalalika a ku Yuda kuchokera ku mbali zonse zinai za dziko lapansi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Iye adzaimika mbendera ya amitundu, ndipo adzasonkhanitsa oingitsidwa a Israele, namema obalalika a Yuda, kuchokera kumadera anai a dziko lapansi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Adzakwezera mitundu ya anthu mbendera, ndipo adzasonkhanitsa otayika a ku Israeli; Iye adzasonkhanitsa anthu obalalika a ku Yuda kuchokera ku mbali zonse zinayi za dziko lapansi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Iye adzaimika mbendera ya amitundu, ndipo adzasonkhanitsa oingitsidwa a Israyeli, namema obalalika a Yuda, kucokera ku madera anai a dziko lapansi.