Isaiah 11:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chilungamo chidzakhala ngati lamba wake, ndipo kukhulupirika, ngati chomangira m'chiwuno mwake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo chilungamo chidzakhala mpango wa m'chuuno mwake, ndi chikhulupiriko chidzakhala mpango wa pa zimpso zake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chilungamo chidzakhala ngati lamba wake ndipo kukhulupirika kudzakhala ngati chomangira mʼchiwuno mwake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo cilungamo cidzakhala mpango wa m'cuuno mwace, ndi cikhulupiriko cidzakhala mpango wa pa zimpsyo zace.