Isaiah 12:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Fuulani ndi kuimba mokondwa, inu anthu a ku Ziyoni, pakuti Woyera Uja wa Israele ndi wamkulu pakati panu.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Tafuula, takuwa iwe, wokhala m'Ziyoni, chifukwa Woyera wa Israele wa m'kati mwako ali wamkulu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Fuwulani ndi kuyimba mwachimwemwe, inu anthu a ku Ziyoni; pakuti Woyerayo wa Israeli ndi wamkulu pakati panu.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Tapfuula, takuwa iwe, wokhala m'Ziyoni, cifukwa Woyera wa Israyeli wa m'kati mwako ali wamkuru.