Isaiah 13:1 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nawu uthenga wonena za Babiloni umene Yesaya, mwana wa Amozi, adalandira kwa Mulungu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Katundu wa Babiloni, imene anaiona Yesaya mwana wa Amozi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Uthenga onena za Babuloni umene Yesaya mwana wa Amozi anawulandira:
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Katundu wa Babulo, imene anaiona Yesaya mwana wa Amozi.