Isaiah 13:18 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adzapha anyamata ndi mauta ao. Sadzachitira chifundo ana. Mitima yao siidzamva chisoni ndi ana akhanda omwe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mauta ao adzatha anyamata; ndipo sadzachitira chisoni chipatso cha mimba; diso lao silidzaleka ana.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Adzapha anyamata ndi mauta awo; sadzachitira chifundo ana ngakhale kumvera chisoni ana akhanda.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mauta ao adzatha anyamata; ndipo sadzacitira cisoni cipatso ca mimba; diso lao silidzaleka ana.