Isaiah 13:2 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kwezani mbendera yankhondo pa phiri loti see. Muŵafuulire ankhondo ndi kuŵakodola kuti adzaloŵe pa zipata za mzinda.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kwezani mbendera pa phiri loti see, kwezani mau kwa iwo, kodolani kuti alowe m'zipata za akulu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kwezani mbendera yankhondo pa phiri loti see, muwafuwulire ankhondo; muwakodole kuti adzalowe pa zipata za anthu olemekezeka.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kwezani mbendera pa phiri loti se, kwezani mau kwa iwo, kodolani kuti alowe m'zipata za akuru.