Isaiah 13:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono manja onse adzafooka, ndipo mtima wa munthu aliyense udzachokamo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa chake manja onse adzafooka, ndi mitima yonse ya anthu idzasungunuka;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Zimenezi zinafowoketsa manja onse, mtima wa munthu aliyense udzachokamo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa cace manja onse adzafoka, ndi mitima yonse ya anthu idzasungunuka;