Isaiah 13:9 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Zoonadi, tsiku la Chauta likudza, tsiku lopanda chisoni, laukali ndi lamkwiyo. Chauta akubwera kuti asandutse dziko lapansi chipululu ndi kuwononga anthu ochimwa am'menemo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Taonani tsiku la Yehova lidza, lankhanza, ndi mkwiyo ndi kukalipira kwaukali; kupasula dziko, ndi kudzaonongamo akuchimwa psiti.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Taonani, tsiku la Yehova likubwera, tsiku lopanda chisoni, lawukali ndi lamkwiyo; kudzasandutsa dziko kuti likhale chipululu ndi kuwononga anthu ochimwa a mʼmenemo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Taonani tsiku la Yehova lidza, lankhanza, ndi mkwiyo ndi kukalipira kwaukali; kupasula dziko, ndi kudzaonongamo akucimwa psiti.