Isaiah 14:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Onsewo adzalankhula, ndipo adzakuuza kuti: ‘Iwenso watheratu mphamvu monga ife! Tsopano tafanana.’
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Onse adzavomera, nadzati kwa iwe, Kodi iwe wakhalanso wopanda mphamvu ngati ife? Kodi iwe wafanana nafe?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Onse adzayankha; adzanena kwa iwe kuti, “Iwenso watheratu mphamvu ngati ife; Iwe wafanana ndi ife.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Onse adzabvomera, nadzati kwa iwe, Kodi iwe wakhalanso wopanda mphamvu ngati ife? kodi iwe wafanana nafe?