Isaiah 14:17 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kodi si ameneyu uja adasandutsa dziko lapansi chipululu ndi kugwetsa mizinda, ndipo sankalola kuti anthu ogwidwa abwerere kwao?’
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
amene anapululutsa dziko, napasula midzi yake, amene sanamasule ndende zake, zinke kwao?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
munthu amene anasandutsa dziko lonse chipululu, amene anagwetsa mizinda yake ndipo sankalola kuti anthu ogwidwa abwerere kwawo?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
amene anapululutsa dziko, napasula midzi yace, amene sanamasula ndende zace, zinke kwao?