Isaiah 14:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta wathyola mkwapulo wa anthu oipa, wasakaza ndodo yaufumu ya olamulira.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Yehova wathyola mkunkhu wa woipa, ndodo yachifumu ya wolamulira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehova wathyola chikwapu cha anthu oyipa, Iye waphwanya ndodo ya olamulira.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Yehova watyola mkunkhu wa woipa, ndodo yacifumu ya wolamulira.