Isaiah 15:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
M'miseu akuvala ziguduli, pamadenga ndi m'mabwalo aliyense akulira kwamphamvu, misozi ili pupupu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
M'makwalala mwao adzimangira chiguduli m'chuuno, pamwamba pa nyumba zao, ndi m'malo a mabwalo ao, yense akuwa, naliritsa kwambiri.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mʼmisewu akuvala ziguduli; pa madenga ndi mʼmabwalo aliyense akulira mofuwula, misozi ili pupupu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
M'makwalala mwao adzimangira ciguduli m'cuuno, pamwamba pa nyumba zao, ndi m'malo a mabwalo ao, yense akuwa, naliritsa kwambiri.