Isaiah 15:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nchifukwa chake anthu akuthaŵa atanyamula chuma chao. Afuna kuwoloka nacho Chigwembe cha Misondodzi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa chake zochuluka adazipeza, ndi zosungidwa zao adzazitenga kunka nazo kumtsinje wa mabango.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kotero kuti chuma chomwe anachipeza ndi kuchisunga, achitenga kuti awoloke nacho chigwembe cha Misondozi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa cace zocuruka adazipeza, ndi zosungidwa zao adzazitenga kunka nazo ku mtsinje wa mabango.