Isaiah 16:11 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nchifukwa chake moyo wanga ukulira ngati pangwe, kulira Mowabu, mtima wanga ukubuula chifukwa cha kuwonongeka kwa Kiriheresi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa chake m'mimba mwanga mulirira Mowabu, ngati mngoli, ndi za m'mtima mwanga zilirira Kiriheresi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chifukwa chake moyo wanga ukulira ngati pangwe kulirira Mowabu, mtima wanga ukubuwula chifukwa cha Kiri Hareseti.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa cace m'mimba mwanga mulirira Moabu, ngati mngoli, ndi za m'mtima mwanga zilirira Kiriheresi.