Isaiah 16:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Monga momwe mbalame zimaulukira uku ndi uku akazimwaza m'chisa, momwemonso akazi a ku Mowabu akuyendayenda ku madooko a Arinoni.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti ana akazi a Mowabu adzakhala pa madooko a Arinoni, ngati mbalame zoyendayenda, ngati chisa chofwanchuka.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Monga momwe mbalame zimawulukira uku ndi uku akazimwaza mʼchisa, momwemonso akazi a ku Mowabu akuyendayenda ku madooko a Arinoni.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti ana akazi a Moabu adzakhala pa madooko a Arinoni, ngati mbalame zoyendayenda, ngati cisa cofwancuka.