Isaiah 17:1 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nawu ulosi wonena za Damasiko: “Mzinda wa Damasiko sudzakhalanso mzinda, koma udzasanduka bwinja.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Katundu wa Damasiko. Taonani, Damasiko wachotsedwa usakhalenso mudzi, ndimo udzangokhala muunda wopasudwa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Uthenga wonena za Damasiko: “Taonani, mzinda wa Damasiko sudzakhalanso mzinda, koma udzasanduka bwinja.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Katundu wa Damasiko. Taonani, Damasiko wacotsedwa usakhalenso mudzi, ndimo udzangokhala muunda wopasudwa.