Isaiah 17:12 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ha, anthu a mitundu yambiri akusokosa kwambiri! Phokoso lao lili ngati kukokoma kwa nyanja! Ha, lumbwe la anthu a mitundu ina, likusokosa ngati madzi amphamvu!
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ha, phokoso la mitundu yambiri ya anthu ambiri, amene afuula ngati kukukuma kwa nyanja; ndi kuthamanga kwa amitundu, akuthamanga ngati kuthamanga kwa madzi amphamvu!
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Aa, mkokomo wa anthu a mitundu yambiri, akusokosa ngati kukokoma kwa nyanja! Aa, phokoso la anthu a mitundu ina, akusokosa ngati mkokomo wa madzi amphamvu!
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ha, phokoso la mitundu yambiri ya anthu ambiri, amene apfuula ngati kukukuma kwa nyanja: ndi kuthamanga kwa amitundu, akuthamanga ngati kuthamangakwa madzi amphamvu!