Isaiah 17:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsiku limenelo anthu adzayang'ana Mlengi wao, ndipo adzatembenukira kwa Woyera uja wa Israele, kufuna thandizo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Tsiku limenelo munthu adzayang'ana kwa Mlengi wake, ndipo maso ake adzalemekeza Woyera wa Israele.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsiku limenelo anthu adzayangʼana Mlengi wawo ndipo adzatembenukira kwa Woyerayo wa Israeli.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Tsiku limenelo munthu adzayang'ana kwa Mlengi wace, ndipo maso ace adzalemekeza Woyera wa Israyeli.