Isaiah 18:1 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsoka kwa anthu okhala ku dziko la patsidya pa mitsinje ya Etiopiya! Kumeneko kumamveka mkokomo wa mapiko.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ha, dziko lakukupuza mapiko, lili tsidya lija la nyanja za Etiopiya;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsoka kwa anthu a ku Kusi. Kumeneko kumamveka mkokomo wa mapiko a dzombe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ha, dziko lakukupuza mapiko, liri tsidya lija la nyanja za Etiopia;