Isaiah 18:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pakuti Chauta adandiwuza kuti, “Kumene ndili Ineko, ndidzangoyang'ana pansi mwakachetechete, monga m'mene dzuŵa limaŵalira nthaŵi yotentha, monganso m'mene amagwera mame usiku pa nthaŵi yakholola.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti Yehova watero kwa ine, Ine ndidzakhala chete, ndipo ndidzayang'ana mokhala chete, ndipo ndidzayang'ana mokhalamo Ine, monga kuwala kotentha kwa dzuwa, monga mtambo wa mame m'kutentha kwa masika.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti Yehova akunena kwa ine kuti, “Ndili chikhalire ku malo anga kuno, ndidzakhala chete, ndi kumangoyangʼana, monga momwe dzuwa limawalira nthawi yotentha, monganso momwe mame amagwera usiku pa nthawi yotentha yokolola.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti Yehova watero kwa ine, Ine ndidzakhala cete, ndipo ndidzayang'ana mokhala cete, ndipo ndidzayang'ana mokhalamo Ine, monga kuwala kotentha kwa dzuwa, monga mtambo wa mame m'kutentha kwa masika.