Isaiah 19:11 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Akalonga a mu mzinda wa Zowani ndi zitsilu. Aphungu anzeru a Farao amalangiza zopusa. Kodi mungathe kumuuza bwanji Farao kunena kuti, “Ine ndine mmodzi mwa anthu anzeru, wophunzira wa mafumu akale?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Akalonga a Zowani apusa ndithu; uphungu wa aphungu anzeru a Farao wasanduka wopulukira; bwanji iwe unena kwa Farao, Ine ndine mwana wa anzeru, mwana wa mafumu akale?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Akuluakulu a ku Zowani ndi zitsiru; aphungu a nzeru a Farao amalangiza zopusa. Kodi mungathe kunena bwanji kwa Farao kuti, “Ine ndine mmodzi mwa anthu anzeru, wophunzira wa mafumu akale?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Akalonga a Zoani apusa ndithu; uphungu wa aphungu anzeru a Farao wasanduka wopulukira; bwanji iwe unena kwa Farao, Ine ndine mwana wa anzeru, mwana wa mafumu akale?