Isaiah 19:15 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo palibe wina aliyense mu Ejipito amene angachitepo kanthu, wolemera kapena wosauka, wotchuka kapena munthu wamba.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ejipito sadzakhala ndi ntchito, imene mutu pena mchira, pena nthambi ya kanjedza, pena mlulu zidzaigwira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Palibe chimene munthu wa mu Igupto angachite, mtsogoleri kapena wotsatira, nthambi ya kanjedza kapena bango.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Aigupto sadzakhala ndi nchito, imene mutu pena mcira, pena nthambi ya kanjedza, pena mlulu zidzaigwira.