Isaiah 19:25 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta Wamphamvuzonse adzaŵadalitsa ndi mau aŵa akuti, “Adalitsidwe Aejipito, anthu anga; adalitsidwe Aasiriya, ntchito ya manja anga; adalitsidwe Aisraele, osankhidwa anga.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
pakuti Yehova wa makamu wadalitsa iwo, ndi kuti, Odalitsika Ejipito anthu anga, ndi Asiriya ntchito ya manja anga, ndi Israele cholowa changa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehova Wamphamvuzonse adzawadalitsa, ndi mawu awa, “Adalitsike anthu anga Aigupto, Aasiriya, ntchito ya manja anga, ndi Aisraeli osankhidwa anga.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
pakuti Yehova wa makamu wadalitsa iwo, ndi kuti, Odalitsika Aigupto anthu anga, ndi Asuri nchito ya manja anga, ndi Israyeli colowa canga.