Isaiah 19:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Madzi a mtsinje wa Nailo adzaphwa, ndipo mtsinjewo udzauma kuchita kuti gwaa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo madzi adzaphwa m'nyanja yaikulu, ndipo nyanja yoyendamo madzi idzaphwa, niuma.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Madzi a mu mtsinje wa Nailo adzaphwa, ndipo mʼmbali mwa mtsinje mudzangʼaluka ndi kuwuma.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo madzi adzaphwa m'nyanja yaikuru, ndipo nyanja yoyendamo madzi idzaphwa, niuma.