Isaiah 19:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ngalande zake zizidzanunkha, ndipo mphanda za mtsinjewo ku Ejipito zidzayamba kuchepa kenaka nkuuma. Bango ndi mlulu zidzafota,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo nyanja zidzanunkha; mitsinje ya Ejipito idzachepa, nuima; bango ndi mlulu zidzafota.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngalande zake zidzanunkha; ndipo mitsinje ya Igupto idzayamba kuchepa ndi kuwuma. Bango ndi dulu zidzafota,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo nyanja zidzanunkha; mitsinje ya Aigupto idzacepa, niuma; bango ndi mlulu zidzafota.