Isaiah 19:9 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu ogwira ntchito yopota thonje, ndiponso anthu oomba nsalu zoyera, adzataya mtima.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Komanso iwo amene agwira ntchito yakupala thonje, ndi iwo amene aomba nsalu yoyera, adzakhala ndi manyazi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Amene amagwira ntchito yopota thonje adzataya mtima, anthu oluka nsalu zofewa zabafuta adzataya chiyembekezo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Komanso iwo amene agwira nchito yakupala bwazi, ndi iwo amene aomba nsaru yoyera, adzakhala ndi manyazi.