Isaiah 2:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Loŵani m'matanthwe, bisalani m'maenje kuti muthaŵe mkwiyo wa Chauta, muthaŵenso ulemerero wa ufumu wake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Lowa m'phanga, bisala m'fumbi, kuchokera pa kuopsa kwa Yehova, ndi pa ulemerero wachifumu wake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Lowani mʼmatanthwe, bisalani mʼmaenje, kuthawa kuopsa kwa Yehova ndi ulemerero wa ufumu wake!
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Lowa m'phanga, bisala m'pfumbi, kucokera pa kuopsya kwa Yehova, ndi pa ulemerero wacifumu wace.