Isaiah 2:13 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adzadula mikungudza yonse ya ku Lebanoni, italiitali kopambana ina yonse. Adzalikha mitengo yonse ya thundu ya ku Basani.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi pa mitengo yonse yamkungudza ya Lebanoni, yaitali ndi yotukulidwa, ndi pa mitengo yonse yathundu ya Basani;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
tsiku la mikungudza yonse ya ku Lebanoni, yayitali ndi yoonekera patali, ndiponso la mitengo yonse ya thundu ya ku Basani,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi pa mitengo yonse yamkungudza ya Lebano, yaitari ndi yotukulidwa, ndi pa mitengo yonse yathundu ya Basana;