Isaiah 2:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Dziko lao nlodzaza ndi mafano. Iwo amapembedza mafano opanga ndi manja ao, oumba ndi zala zao zomwe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Dziko lao ladzalanso mafano; iwo apembedza ntchito ya manja aoao, imene zala zaozao zinaipanga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Dziko lawo ndi lodzaza ndi mafano; iwo amapembedza ntchito ya manja awo, amagwadira zomwe anapanga ndi zala zawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Dziko lao ladzalanso mafano; iwo apembedza nchito ya manja ao ao, imene zala zao zao zinaipanga.