Isaiah 20:1 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chaka china mtsogoleri wankhondo wotumidwa ndi Sarigoni, mfumu ya ku Asiriya, adaadzalimbana ndi mzinda wa Asidodi, naulanda.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chaka chimene kazembe wa ku Asiriya anafika ku Asidodi, muja Sarigoni mfumu ya Asiriya anamtumiza iye, ndipo iye anamenyana ndi Asidodi, naugonjetsa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mʼchaka chimene mkulu wankhondo wotumidwa ndi mfumu ya ku Asiriya, anabwera ku Asidodi ndi kuwuthira nkhondo ndi kuwulanda,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Caka cimene kazembe wa ku Asuri anafika ku Asidodi, muja Sarigoni mfumu ya Asuri anamtumiza iye, ndipo iye anamenyana ndi Asidodi, naugonjetsa.