Isaiah 20:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono onse amene ankadalira dziko la Etiopiya ndiponso amene ankakhulupirira Ejipito, adzamva chisoni ndi kuchita manyazi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo iwo adzakhala ndi mantha ndi manyazi, chifukwa cha Kusi, amene anawatama, ndi Ejipito, amene anawanyadira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Amene ankadalira Kusi, ndiponso amene ankadzitukumula chifukwa cha Igupto adzakhumudwa ndi kuchita manyazi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo iwo adzakhala ndi mantha ndi manyazi, cifukwa ca Kusi, amene anawatama, ndi Aigupto, amene anawanyadira.