Isaiah 21:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndiye abale anga Aisraele, inu opunthidwa ndi opetedwa ngati tirigu, tsopano ndakuuzani uthenga umene ndamva kwa Chauta Wamphamvuzonse, Mulungu wa Israele.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kuomba kwanga nanga, ndi za pa dwale langa: chimene ine ndinachimva kwa Yehova wa makamu Mulungu wa Israele, ndanena kwa inu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Inu anthu anga opunthidwa ndi kupetedwa ngati tirigu, ine ndikukuwuzani zimene ndamva ndikukuwuzani Uthenga wochokera kwa Yehova Wamphamvuzonse, Mulungu wa Israeli.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kuomba kwanga nanga, ndi za pa dwale langa: cimene ine ndinacimva kwa Yehova wa makamu Mulungu wa Israyeli, ndanena kwa inu.