Isaiah 21:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mlonda akuti, “Kulikucha, koma kudanso. Ukafuna kufunsanso, ubwerenso udzafunse.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mlonda anati, Kuli kucha, koma kukali usiku; mukafuna kufunsa, funsani, bwerani, idzani.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mlonda akuyankha kuti, “Kukucha, koma kudanso. Ngati ukufuna kufunsa, funsa tsopano; ndipo ubwerenso udzafunse.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mlonda anati, Kuli kuca, koma kukali usiku; mukafuna kufunsa, funsani, bwerani, idzani.