Isaiah 21:13 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nawu ulosi wonena za Arabiya: Inu anthu a ku Dedani oyenda pa gulu, amene usiku mumagona m'malunje a ku Arabiya,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Katundu wa pa Arabiya. M'nkhalango ya m'Arabiya mudzagona, inu makamu oyendayenda a Dedani.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Uthenga wonena za Arabiya: Inu anthu amalonda a ku Dedani, amene usiku mumagona mʼzithukuluzi za ku Arabiya,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Katundu wa pa Arabiya. M'nkhalango ya m'Arabiya mudzagona, inu makamu oyendayenda a Dedani.