Isaiah 21:14 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
muŵapatse madzi anthu aludzu kuti amwe. Inu anthu a ku Tema, muŵapatse chakudya anthu othaŵa nkhondo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Muchingamire akumva ludzu ndi madzi; okhala m'dziko la Tema ananka kukomana ndi othawa ndi chakudya chao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
perekani madzi kwa anthu aludzu. Inu anthu a ku Tema perekani chakudya kwa anthu othawa nkhondo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mucingamire akumva ludzu ndi madzi; okhala m'dziko la Tema ananka kukomana ndi othawa ndi cakudya cao.