Isaiah 21:15 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pakuti akuthaŵa malupanga, malupanga osololasolola, mauta okokakoka, ndiponso nkhondo yoopsa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti iwo anathawa malupanga, malupanga osololedwa, ndi mauta olifuka ndi nkhondo yovuta.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo akuthawa malupanga, lupanga losololedwa, akuthawa uta wokokakoka ndiponso nkhondo yoopsa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti iwo anathawa malupanga, malupanga osololedwa, ndi mauta-olifuka ndi nkhondo yobvuta.