Isaiah 21:16 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ambuye adandiwuza kuti, “Chatsala chaka chimodzi, potsata m'mene amaŵerengera munthu waganyu, ndipo ulemu wonse wa anthu a ku Kedara udzatheratu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti Ambuye anatero kwa ine, Chisanapite chaka malinga ndi zaka za wolembedwa ntchito, ulemerero wonse wa Kedara udzagoma;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Zimene Ambuye akunena kwa ine ndi izi: “Chaka chimodzi chisanathe, potsata mmene amawerengera munthu waganyu, ulemerero wonse wa Kedara udzatheratu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti Ambuye ana tero kwa ine, Cisanapite caka malinga ndi zaka za wolembedwa nchito ulemerero wonse wa Kedara udzagoma;