Isaiah 21:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pakuti Ambuye andiwuza kuti, “Pita, kaike mlonda kuti azinena zimene akuwona.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti Ambuye atero kwa ine, Muka, ika mlonda anene chimene achiona;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Zimene Ambuye akunena kwa ine ndi izi; “Pita, kayike mlonda kuti azinena zimene akuziona.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti Ambuye atero kwa ine, Muka, ika mlonda anene cimene aciona;